Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Oyimba ambiri ku Malawi alibe mwayi okuti nyimbo zawo ziziseweledwa kunja

View descriptionShare

Kafukufuku yemwe wailesi ya channel africa yachita yapeza kuti oimba nyimbo ambiri am'dziko la Malawi alibe kuthekera koti nyimbo zawo mkumaseweredwa mmawailesi ndi ma kanema ammaiko akunja kwa dzikolo zomwe zikuchititsa kuti oimbawa tsogolo lawo lamaimbidwe awo lisamaoneke bwinobwino.

Mtolankhani mzathu mu nzinda wa Lilongwe mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • Twitter
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    463 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 600 clip(s)